Kulima Gender Comic Book-Kabuku ka Mchezo

14.10.2022

Buku la m’chezoli pa nkhani zoona kusasiyina pakati pa amayi ndi abambo lakonzedwa ndi bungwe la Self Help Africa mogwirizana ndi mabungwe awa; Actionaid International Malawi, Adventist Development Relief Agency, Evangelical Association of Malawi komanso Plan International Malawi, ndi thandizo la ndalama kuchokera ku European Union.